Miyambo 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Amene akufunafuna chilungamo+ ndiponso kukoma mtima kosatha adzapeza moyo, chilungamo ndi ulemerero.+ Yesaya 26:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Njira ya munthu wolungama ndi yowongoka.+ Popeza inu ndinu wochita zowongoka, mudzasalaza njira ya munthu wolungama.+ Yohane 3:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Atate amakonda Mwana wake+ ndipo anapereka zinthu zonse m’manja mwake.+
21 Amene akufunafuna chilungamo+ ndiponso kukoma mtima kosatha adzapeza moyo, chilungamo ndi ulemerero.+
7 Njira ya munthu wolungama ndi yowongoka.+ Popeza inu ndinu wochita zowongoka, mudzasalaza njira ya munthu wolungama.+