Miyambo 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova amanyansidwa ndi njira ya munthu woipa,+ koma iye amakonda munthu wochita chilungamo.+ Mateyu 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Odala ndi anthu amene akumva njala ndi ludzu+ la chilungamo, chifukwa adzakhuta.+ Aheberi 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yesetsani kukhala pa mtendere ndi anthu onse,+ komanso yesetsani kukhala oyera+ chifukwa ngati munthu si woyera, sadzaona Ambuye.+
14 Yesetsani kukhala pa mtendere ndi anthu onse,+ komanso yesetsani kukhala oyera+ chifukwa ngati munthu si woyera, sadzaona Ambuye.+