Mateyu 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano mayi wina amene anali ndi nthenda yotaya magazi kwa zaka 12+ anafika kumbuyo kwake n’kugwira ulusi wopota wa m’mphepete mwa malaya ake akunja,+ Maliko 5:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsopano panali mayi wina amene anali ndi nthenda yotaya magazi+ kwa zaka 12,+
20 Tsopano mayi wina amene anali ndi nthenda yotaya magazi kwa zaka 12+ anafika kumbuyo kwake n’kugwira ulusi wopota wa m’mphepete mwa malaya ake akunja,+