Mateyu 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano mayi wina amene anali ndi nthenda yotaya magazi kwa zaka 12+ anafika kumbuyo kwake n’kugwira ulusi wopota wa m’mphepete mwa malaya ake akunja,+ Luka 8:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Ndiyeno panali mayi wina amene anali ndi nthenda yotaya magazi+ kwa zaka 12, ndipo palibe aliyense amene anatha kum’chiritsa.+
20 Tsopano mayi wina amene anali ndi nthenda yotaya magazi kwa zaka 12+ anafika kumbuyo kwake n’kugwira ulusi wopota wa m’mphepete mwa malaya ake akunja,+
43 Ndiyeno panali mayi wina amene anali ndi nthenda yotaya magazi+ kwa zaka 12, ndipo palibe aliyense amene anatha kum’chiritsa.+