Yesaya 49:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kodi anthu amene atengedwa kale angalandidwe m’manja mwa munthu wamphamvu,+ kapena kodi gulu la anthu amene agwidwa ndi wolamulira wankhanza lingathawe?+ Mateyu 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kapena munthu angalowe bwanji m’nyumba ya munthu wamphamvu ndi kulanda katundu wake, ngati sangamange munthu wamphamvuyo choyamba? Atam’manga, m’pamene angathe kutenga katundu m’nyumbamo.+ Maliko 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kunena zoona, palibe amene angalowe m’nyumba ya munthu wamphamvu ndi kulanda+ katundu wake ngati sangamange munthu wamphamvuyo choyamba. Atam’manga, m’pamene angathe kutenga katundu m’nyumbamo.+
24 Kodi anthu amene atengedwa kale angalandidwe m’manja mwa munthu wamphamvu,+ kapena kodi gulu la anthu amene agwidwa ndi wolamulira wankhanza lingathawe?+
29 Kapena munthu angalowe bwanji m’nyumba ya munthu wamphamvu ndi kulanda katundu wake, ngati sangamange munthu wamphamvuyo choyamba? Atam’manga, m’pamene angathe kutenga katundu m’nyumbamo.+
27 Kunena zoona, palibe amene angalowe m’nyumba ya munthu wamphamvu ndi kulanda+ katundu wake ngati sangamange munthu wamphamvuyo choyamba. Atam’manga, m’pamene angathe kutenga katundu m’nyumbamo.+