Machitidwe 7:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Ndi mneneri uti amene makolo anuwo sanamuzunze?+ Inde, iwo anapha+ amene analengezeratu za kubwera kwa Wolungamayo,+ amene inuyo munamupereka ndi kumupha,+ Aheberi 11:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Anaponyedwa miyala,+ anayesedwa,+ anachekedwa pakati ndi macheka, anaphedwa+ mwankhanza ndi lupanga, anayendayenda atavala zikopa za nkhosa+ ndi zikopa za mbuzi pamene anali osowa,+ pamene anali m’masautso+ komanso pamene anali kuzunzidwa.+
52 Ndi mneneri uti amene makolo anuwo sanamuzunze?+ Inde, iwo anapha+ amene analengezeratu za kubwera kwa Wolungamayo,+ amene inuyo munamupereka ndi kumupha,+
37 Anaponyedwa miyala,+ anayesedwa,+ anachekedwa pakati ndi macheka, anaphedwa+ mwankhanza ndi lupanga, anayendayenda atavala zikopa za nkhosa+ ndi zikopa za mbuzi pamene anali osowa,+ pamene anali m’masautso+ komanso pamene anali kuzunzidwa.+