Mateyu 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mofanana ndi zimenezi inunso, pamaso pa anthu, mumaonekadi ngati olungama+ koma mkati mwanu mwadzaza chinyengo ndi kusamvera malamulo. Luka 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa nthawiyi, chikhamu cha anthu masauzandemasauzande chinali chitasonkhana, moti anali kupondanapondana. Pamenepo Yesu anayamba kulankhula ndi ophunzira ake choyamba kuti: “Samalani ndi chofufumitsa+ cha Afarisi, chimene chili chinyengo.+
28 Mofanana ndi zimenezi inunso, pamaso pa anthu, mumaonekadi ngati olungama+ koma mkati mwanu mwadzaza chinyengo ndi kusamvera malamulo.
12 Pa nthawiyi, chikhamu cha anthu masauzandemasauzande chinali chitasonkhana, moti anali kupondanapondana. Pamenepo Yesu anayamba kulankhula ndi ophunzira ake choyamba kuti: “Samalani ndi chofufumitsa+ cha Afarisi, chimene chili chinyengo.+