1 Petulo 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Khalani ndi chikumbumtima chabwino,+ kuti ngakhale azikunenerani zoipa ndi kulankhula monyoza za khalidwe lanu labwino monga otsatira Khristu, adzachite manyazi.+
16 Khalani ndi chikumbumtima chabwino,+ kuti ngakhale azikunenerani zoipa ndi kulankhula monyoza za khalidwe lanu labwino monga otsatira Khristu, adzachite manyazi.+