Yohane 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma pamene ansembe aakulu ndi alonda anamuona, anafuula kuti: “M’pachikeni! M’pachikeni!”+ Pilato anawauza kuti: “M’tengeni mukamupachike nokha, chifukwa ine sindikupeza mlandu uliwonse mwa iye.”+ Machitidwe 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ngati nkhani yake ili yokhudza mikangano pa mawu, mayina+ ndi chilamulo+ chanu, zimenezo muthane nazo nokha. Ine sindikufuna kuti ndikhale woweruza nkhani zoterezi.”
6 Koma pamene ansembe aakulu ndi alonda anamuona, anafuula kuti: “M’pachikeni! M’pachikeni!”+ Pilato anawauza kuti: “M’tengeni mukamupachike nokha, chifukwa ine sindikupeza mlandu uliwonse mwa iye.”+
15 Koma ngati nkhani yake ili yokhudza mikangano pa mawu, mayina+ ndi chilamulo+ chanu, zimenezo muthane nazo nokha. Ine sindikufuna kuti ndikhale woweruza nkhani zoterezi.”