Luka 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Pilato anauza ansembe aakulu ndi khamu la anthulo kuti: “Sindikupeza mlandu uliwonse mwa munthu uyu.”+ Yohane 18:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pilato anafunsa kuti: “Choonadi n’chiyani?” Atangofunsa funso limeneli, anatuluka ndi kupitanso kumene kunali Ayuda kuja, ndi kuwauza kuti: “Ineyo sindikupeza cholakwa chilichonse mwa munthu ameneyu.+ 2 Akorinto 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Amene analibe uchimoyo,+ Mulungu anamupanga kukhala uchimo+ chifukwa cha ife, kuti tikhale olungama pamaso pa Mulungu+ kudzera mwa iye.
4 Pamenepo Pilato anauza ansembe aakulu ndi khamu la anthulo kuti: “Sindikupeza mlandu uliwonse mwa munthu uyu.”+
38 Pilato anafunsa kuti: “Choonadi n’chiyani?” Atangofunsa funso limeneli, anatuluka ndi kupitanso kumene kunali Ayuda kuja, ndi kuwauza kuti: “Ineyo sindikupeza cholakwa chilichonse mwa munthu ameneyu.+
21 Amene analibe uchimoyo,+ Mulungu anamupanga kukhala uchimo+ chifukwa cha ife, kuti tikhale olungama pamaso pa Mulungu+ kudzera mwa iye.