Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 45:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Chotero si inu amene munanditumiza kuno,+ koma Mulungu woona. Anachita zimenezi kuti andiike kukhala tate+ kwa Farao, ndi mbuye wa nyumba yake yonse, ndiponso woyang’anira wa dziko lonse la Iguputo.

  • Danieli 4:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Alonda+ ndi amene alamula zimenezi. Angelo oyera* ndi amene apempha zimenezi ndi cholinga chakuti anthu adziwe kuti Wam’mwambamwamba ndiye Wolamulira wa maufumu a anthu,+ ndiponso adziwe kuti iye akafuna kupereka ulamuliro kwa munthu aliyense, amamupatsa+ ndipo amaika ngakhale munthu wonyozeka kwambiri kuti azilamulira.”+

  • Luka 22:53
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 53 Tsiku ndi tsiku ndinali nanu m’kachisi+ koma simunandigwire.+ Koma ino tsopano ndi nthawi yanu+ komanso nthawi ya ulamuliro+ wa mdima.”+

  • Yohane 7:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Pamenepo anayamba kufufuza njira yomugwirira,+ koma palibe amene anamugwira chifukwa nthawi yake+ inali isanafike.

  • Yohane 10:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Palibe munthu amene akuuchotsa kwa ine, koma ndikuupereka mwa kufuna kwanga. Ndili ndi mphamvu zoupereka, ndiponso ndili ndi mphamvu zoulandiranso.+ Atate wanga ndi amene anandilamula+ kuchita zimenezi.”

  • Aroma 13:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Chotero amene akutsutsana ndi ulamuliro akutsutsana ndi dongosolo la Mulungu. Amene akutsutsana ndi dongosolo limeneli adzalandira chiweruzo.+

  • Chivumbulutso 13:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chinaloledwa+ kuchita nkhondo ndi oyerawo ndi kuwagonjetsa.+ Chinapatsidwanso ulamuliro pa anthu a fuko lililonse, mtundu uliwonse, chinenero chilichonse ndi dziko lililonse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena