Yohane 9:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndiyeno Yesu ananena kuti: “Ndinabwera m’dziko lino kudzapereka chiweruzo ichi:+ Osaona ayambe kuona,+ ndipo oona akhale akhungu.”+ Yohane 12:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndabwera monga kuwala m’dziko,+ kuti aliyense wokhulupirira ine asapitirize kukhala mumdima.+
39 Ndiyeno Yesu ananena kuti: “Ndinabwera m’dziko lino kudzapereka chiweruzo ichi:+ Osaona ayambe kuona,+ ndipo oona akhale akhungu.”+