Yohane 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ine sindingachite chilichonse chongoganiza ndekha. Ndimaweruza malinga ndi mmene ndamvera, ndipo chiweruzo chimene ndimapereka n’cholungama,+ chifukwa sinditsatira chifuniro changa, koma chifuniro+ cha amene anandituma. Yohane 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamenepo Yesu anati: “Mukadzamukweza+ Mwana wa munthu,+ pamenepo mudzadziwa kuti ine ndine amene munali kumuyembekezera uja,+ ndi kutinso sindichita kanthu mongoganiza ndekha.+ Koma ndimalankhula zinthu izi ndendende mmene Atate anandiphunzitsira.+ Yohane 12:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Chifukwa sindinalankhulepo zongoganiza pandekha, koma Atate amene ananditumawo anandipatsa lamulo pa zimene ndiyenera kunena ndi zimene ndiyenera kulankhula.+
30 Ine sindingachite chilichonse chongoganiza ndekha. Ndimaweruza malinga ndi mmene ndamvera, ndipo chiweruzo chimene ndimapereka n’cholungama,+ chifukwa sinditsatira chifuniro changa, koma chifuniro+ cha amene anandituma.
28 Pamenepo Yesu anati: “Mukadzamukweza+ Mwana wa munthu,+ pamenepo mudzadziwa kuti ine ndine amene munali kumuyembekezera uja,+ ndi kutinso sindichita kanthu mongoganiza ndekha.+ Koma ndimalankhula zinthu izi ndendende mmene Atate anandiphunzitsira.+
49 Chifukwa sindinalankhulepo zongoganiza pandekha, koma Atate amene ananditumawo anandipatsa lamulo pa zimene ndiyenera kunena ndi zimene ndiyenera kulankhula.+