Yohane 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano pasika+ wa Ayuda anali pafupi. Choncho Yesu ananyamuka kupita ku Yerusalemu.+ Yohane 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pambuyo pa zonsezi, kunali chikondwerero+ cha Ayuda, ndipo Yesu ananyamuka kupita ku Yerusalemu.