Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 8:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Kenako panyanjapo panabuka mphepo yamphamvu moti mafunde anali kulowa m’ngalawamo, koma iye anali m’tulo.+

  • Mateyu 14:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Pa nthawiyi n’kuti ngalawa ija itapita kutali pakati pa madzi, ndipo inali kukankhidwa mwamphamvu ndi mafunde+ chifukwa anali kulimbana ndi mphepo yamphamvu.

  • Maliko 6:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Kenako anaona ophunzirawo akupalasa movutika,+ chifukwa anali kulimbana ndi mphepo yamphamvu. Uwu unali m’bandakucha pafupifupi pa ulonda wachinayi,* ndipo iye anawalondola akuyenda panyanja. Koma ophunzirawo anaona ngati akufuna kuwapitirira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena