Mateyu 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 ndipo adzamupha. Koma pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.”+ Atamva zimenezi iwo anamva chisoni kwambiri.+ Yohane 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Mitima yanu isavutike.+ Khulupirirani Mulungu,+ khulupiriraninso ine.+ Yohane 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho inunso muli ndi chisoni panopa. Koma ndidzakuonaninso, ndipo mitima yanu idzasangalala.+ Palibenso amene adzathetse chimwemwe chanu.
23 ndipo adzamupha. Koma pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.”+ Atamva zimenezi iwo anamva chisoni kwambiri.+
22 Choncho inunso muli ndi chisoni panopa. Koma ndidzakuonaninso, ndipo mitima yanu idzasangalala.+ Palibenso amene adzathetse chimwemwe chanu.