Mateyu 13:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yesu analankhula zonsezi ndi khamu la anthulo m’mafanizo. Ndithudi, sanalankhule nawo chilichonse popanda fanizo,+ Yohane 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yesu ananena fanizoli kwa iwo, koma iwo sanadziwe tanthauzo la zinthu zimene anali kuwauzazo.+
34 Yesu analankhula zonsezi ndi khamu la anthulo m’mafanizo. Ndithudi, sanalankhule nawo chilichonse popanda fanizo,+