Maliko 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 kuti: “Nthawi yoikidwiratu yakwaniritsidwa!+ Ufumu wa Mulungu wayandikira! Lapani+ anthu inu! Khulupirirani uthenga wabwino!” Luka 24:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 ndipo pa maziko a dzina lake, m’mitundu yonse+ mudzalalikidwa za kulapa kuti machimo akhululukidwe.+ Kuyambira ku Yerusalemu+ Machitidwe 2:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Petulo anawayankha kuti: “Lapani,+ ndipo aliyense wa inu abatizidwe+ m’dzina+ la Yesu Khristu kuti machimo anu akhululukidwe.+ Mukatero mudzalandira mphatso yaulere+ ya mzimu woyera.
15 kuti: “Nthawi yoikidwiratu yakwaniritsidwa!+ Ufumu wa Mulungu wayandikira! Lapani+ anthu inu! Khulupirirani uthenga wabwino!”
47 ndipo pa maziko a dzina lake, m’mitundu yonse+ mudzalalikidwa za kulapa kuti machimo akhululukidwe.+ Kuyambira ku Yerusalemu+
38 Petulo anawayankha kuti: “Lapani,+ ndipo aliyense wa inu abatizidwe+ m’dzina+ la Yesu Khristu kuti machimo anu akhululukidwe.+ Mukatero mudzalandira mphatso yaulere+ ya mzimu woyera.