-
Machitidwe 6:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Mwachitsanzo, ife tinamumva iyeyu akunena kuti Yesu Mnazareti uja adzawononga malo oyera ano ndi kusintha miyambo imene Mose anatipatsa.”
-