Machitidwe 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene ndinali kuchita zimenezi, anandipeza m’kachisi nditadziyeretsa monga mwa mwambo,+ koma panalibe khamu la anthu kapena wochita phokoso. Kumeneko kunali Ayuda ena ochokera m’chigawo cha Asia. 1 Akorinto 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Motero kwa Ayuda ndinakhala ngati Myuda,+ kuti ndipindule Ayuda. Kwa anthu otsatira chilamulo+ ndinakhala ngati wotsatira chilamulo+ kuti ndipindule anthu otsatira chilamulo, ngakhale kuti sindili pansi pa chilamulo.
18 Pamene ndinali kuchita zimenezi, anandipeza m’kachisi nditadziyeretsa monga mwa mwambo,+ koma panalibe khamu la anthu kapena wochita phokoso. Kumeneko kunali Ayuda ena ochokera m’chigawo cha Asia.
20 Motero kwa Ayuda ndinakhala ngati Myuda,+ kuti ndipindule Ayuda. Kwa anthu otsatira chilamulo+ ndinakhala ngati wotsatira chilamulo+ kuti ndipindule anthu otsatira chilamulo, ngakhale kuti sindili pansi pa chilamulo.