11 Koma tsiku lomwelo usiku, Ambuye anaimirira pambali pake+ ndi kunena kuti: “Limba mtima!+ Pakuti wandichitira umboni mokwanira+ mu Yerusalemu, ndipo ukandichitiranso umboni ku Roma.”+
16 Komabe, dzuka ndi kuimirira.+ Pakuti ine ndaonekera kwa iwe kuti ndikusankhe kuti ukhale mtumiki ndi mboni+ ya zinthu zonse, zimene waona ndi zimene ndidzakuonetsa zokhudza ine.