Ezekieli 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu,+ imirira kuti ndikulankhule.”+