Machitidwe 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti udzakhala mboni yake kwa anthu onse pa zinthu zimene waona ndi kumva.+ Agalatiya 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Uthengawu sindinaulandire kwa munthu, ndipo sindinachite kuuphunzira mwanjira ina, koma Yesu Khristu ndiye amene anandiululira uthenga umenewu.+ 1 Timoteyo 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndikuyamika Khristu Yesu Ambuye wathu amene anandipatsa mphamvu poona kuti ndine wokhulupirika,+ ndipo anandipatsa utumiki.+
12 Uthengawu sindinaulandire kwa munthu, ndipo sindinachite kuuphunzira mwanjira ina, koma Yesu Khristu ndiye amene anandiululira uthenga umenewu.+
12 Ndikuyamika Khristu Yesu Ambuye wathu amene anandipatsa mphamvu poona kuti ndine wokhulupirika,+ ndipo anandipatsa utumiki.+