Machitidwe 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Saulo anali kuvomereza za kupha Sitefano.+ Tsiku limenelo, panabuka chizunzo chachikulu+ choukira mpingo umene unali mu Yerusalemu. Onse anabalalikira+ m’zigawo za Yudeya ndi Samariya, kupatulapo atumwi okha. 1 Timoteyo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mawu akuti Khristu Yesu anabwera m’dziko kudzapulumutsa ochimwa,+ ndi mawu oona ndi oyenera kuwavomereza ndi mtima wonse.+ Mwa ochimwa amenewa, ine ndiye wochimwa kwambiri.+
8 Ndiyeno Saulo anali kuvomereza za kupha Sitefano.+ Tsiku limenelo, panabuka chizunzo chachikulu+ choukira mpingo umene unali mu Yerusalemu. Onse anabalalikira+ m’zigawo za Yudeya ndi Samariya, kupatulapo atumwi okha.
15 Mawu akuti Khristu Yesu anabwera m’dziko kudzapulumutsa ochimwa,+ ndi mawu oona ndi oyenera kuwavomereza ndi mtima wonse.+ Mwa ochimwa amenewa, ine ndiye wochimwa kwambiri.+