Machitidwe 28:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pa chifukwa chimenechi, ndinapempha kuti ndikuoneni ndi kulankhula nanu, pakuti ndamangidwa ndi unyolo uwu+ chifukwa cha chiyembekezo+ cha Isiraeli.”
20 Pa chifukwa chimenechi, ndinapempha kuti ndikuoneni ndi kulankhula nanu, pakuti ndamangidwa ndi unyolo uwu+ chifukwa cha chiyembekezo+ cha Isiraeli.”