Machitidwe 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano Paulo ataona kuti ena mwa iwo anali Asaduki+ ndipo ena anali Afarisi, anafuula m’khotimo kuti: “Amuna inu, abale anga, ine ndine Mfarisi,+ mwana wa Afarisi. Pano ndikuweruzidwa+ chifukwa cha chiyembekezo cha kuuka+ kwa akufa.” Machitidwe 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma tsopano ndaimirira pano kuti ndiweruzidwe, chifukwa cha chiyembekezo+ pa lonjezo+ limene Mulungu anapereka kwa makolo athu. Tito 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tizichita zimenezi pamene tikuyembekeza kukwaniritsidwa kwa chiyembekezo+ chosangalatsa ndi kuonetsedwa kwaulemerero+ kwa Mulungu wamkuluyo ndiponso kwa Mpulumutsi wathu, Khristu Yesu.
6 Tsopano Paulo ataona kuti ena mwa iwo anali Asaduki+ ndipo ena anali Afarisi, anafuula m’khotimo kuti: “Amuna inu, abale anga, ine ndine Mfarisi,+ mwana wa Afarisi. Pano ndikuweruzidwa+ chifukwa cha chiyembekezo cha kuuka+ kwa akufa.”
6 Koma tsopano ndaimirira pano kuti ndiweruzidwe, chifukwa cha chiyembekezo+ pa lonjezo+ limene Mulungu anapereka kwa makolo athu.
13 Tizichita zimenezi pamene tikuyembekeza kukwaniritsidwa kwa chiyembekezo+ chosangalatsa ndi kuonetsedwa kwaulemerero+ kwa Mulungu wamkuluyo ndiponso kwa Mpulumutsi wathu, Khristu Yesu.