Yesaya 58:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 “Fuula mwamphamvu! Usabweze mawu.+ Kweza mawu ako ngati lipenga,+ ndipo uza anthu anga za kupanduka kwawo. A nyumba ya Yakobo uwauze machimo awo. Machitidwe 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kwa miyezi itatu, anali kupita kusunagoge+ kumene anali kulankhula molimba mtima. Kumeneko anali kukamba nkhani ndi kuwafotokozera mfundo zokhutiritsa zokhudza ufumu+ wa Mulungu.
58 “Fuula mwamphamvu! Usabweze mawu.+ Kweza mawu ako ngati lipenga,+ ndipo uza anthu anga za kupanduka kwawo. A nyumba ya Yakobo uwauze machimo awo.
8 Kwa miyezi itatu, anali kupita kusunagoge+ kumene anali kulankhula molimba mtima. Kumeneko anali kukamba nkhani ndi kuwafotokozera mfundo zokhutiritsa zokhudza ufumu+ wa Mulungu.