Machitidwe 2:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Pamenepo anthu onse anayamba kuchita mantha, ndipo atumwiwo anayamba kuchita zodabwitsa ndi zizindikiro zambiri.+ Machitidwe 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho atumwiwo anapitiriza kuchita zizindikiro ndi zodabwitsa zambiri pakati pa anthu.+ Ndipo okhulupirira onse mogwirizana anali kusonkhana m’khonde la zipilala la Solomo.+
43 Pamenepo anthu onse anayamba kuchita mantha, ndipo atumwiwo anayamba kuchita zodabwitsa ndi zizindikiro zambiri.+
12 Choncho atumwiwo anapitiriza kuchita zizindikiro ndi zodabwitsa zambiri pakati pa anthu.+ Ndipo okhulupirira onse mogwirizana anali kusonkhana m’khonde la zipilala la Solomo.+