Machitidwe 4:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 kudzazipereka kwa atumwi.+ Ndiyeno ndalamazo anali kuzigawa+ kwa aliyense malinga ndi zosowa zake. 1 Timoteyo 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Lemekeza akazi amasiye amene alidi amasiye.+ Yakobo 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kupembedza koyera+ ndi kosaipitsidwa+ kwa Mulungu ndi Atate wathu ndi uku: Kusamalira ana amasiye+ ndi akazi amasiye+ m’masautso awo,+ ndi kukhala wopanda banga+ la dzikoli.+
35 kudzazipereka kwa atumwi.+ Ndiyeno ndalamazo anali kuzigawa+ kwa aliyense malinga ndi zosowa zake.
27 Kupembedza koyera+ ndi kosaipitsidwa+ kwa Mulungu ndi Atate wathu ndi uku: Kusamalira ana amasiye+ ndi akazi amasiye+ m’masautso awo,+ ndi kukhala wopanda banga+ la dzikoli.+