Salimo 81:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho ndinawasiya kuti apitirize kuumitsa mtima wawo.+Iwo anapitiriza kuyenda mu nzeru zawo.+ Aroma 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chotero malinga ndi zilakolako za m’mitima mwawo, Mulungu anawasiya kuti achite zonyansa,+ kuti matupi awo+ achitidwe chipongwe.+ 2 Atesalonika 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ichi n’chifukwa chake Mulungu walola kuti iwo anyengedwe ndipo azikhulupirira bodza,+
24 Chotero malinga ndi zilakolako za m’mitima mwawo, Mulungu anawasiya kuti achite zonyansa,+ kuti matupi awo+ achitidwe chipongwe.+