Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 28:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mwadzidzidzi Yesu anakumana nawo n’kunena kuti: “Moni amayi!” Pamenepo iwo anafika pafupi ndi kugwira mapazi ake ndi kumuweramira mpaka nkhope zawo pansi.

  • Yohane 20:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Pa tsiku limenelo, tsiku loyamba la mlunguwo,+ ophunzirawo anasonkhana pamodzi madzulo. Iwo anali atakhoma zitseko m’nyumba imene analimo chifukwa choopa+ Ayuda, ndipo Yesu anafika+ n’kuimirira pakati pawo ndi kunena kuti: “Mtendere ukhale nanu.”+

  • 1 Akorinto 15:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno anaonekeranso kwa abale oposa 500 pa nthawi imodzi, ndipo ambiri a iwo akali ndi moyo mpaka lero,+ koma ena anagona mu imfa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena