Ezekieli 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 M’chaka cha 30, m’mwezi wachinayi, pa tsiku lachisanu la mweziwo, pamene ndinali pakati pa anthu amene anali ku ukapolo+ pafupi ndi mtsinje wa Kebara,+ kumwamba kunatseguka+ ndipo ndinayamba kuona masomphenya a Mulungu.+ Mateyu 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atabatizidwa, nthawi yomweyo Yesu anavuuka m’madzimo. Pamenepo kumwamba kunatseguka,+ ndipo Yohane anaona mzimu wa Mulungu ukutsika ngati nkhunda+ kudzamutera.+ Yohane 1:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Anamuuzanso kuti: “Ndithudi ndikukuuzani anthu inu, mudzaona kumwamba kutatseguka, angelo+ a Mulungu akukwera ndi kutsikira kwa Mwana wa munthu.”+
1 M’chaka cha 30, m’mwezi wachinayi, pa tsiku lachisanu la mweziwo, pamene ndinali pakati pa anthu amene anali ku ukapolo+ pafupi ndi mtsinje wa Kebara,+ kumwamba kunatseguka+ ndipo ndinayamba kuona masomphenya a Mulungu.+
16 Atabatizidwa, nthawi yomweyo Yesu anavuuka m’madzimo. Pamenepo kumwamba kunatseguka,+ ndipo Yohane anaona mzimu wa Mulungu ukutsika ngati nkhunda+ kudzamutera.+
51 Anamuuzanso kuti: “Ndithudi ndikukuuzani anthu inu, mudzaona kumwamba kutatseguka, angelo+ a Mulungu akukwera ndi kutsikira kwa Mwana wa munthu.”+