Machitidwe 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma iye anawakwezera dzanja+ kuti akhale chete, ndipo anawafotokozera mwatsatanetsatane mmene Yehova anamutulutsira m’ndende. Kenako iye anati: “Zinthu zimenezi mukazifotokoze kwa Yakobo+ ndi kwa abale.” Atatero anatuluka n’kupita kumalo ena. Machitidwe 21:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Atamulola, Paulo anaimirira pamasitepe ndi kukwezera anthuwo dzanja.+ Onse atakhala phee, analankhula nawo m’Chiheberi,+ kuti: Machitidwe 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno Agiripa+ anauza Paulo kuti: “Waloledwa kulankhula mbali yako.” Pamenepo Paulo anatambasula dzanja lake+ ndi kuyamba kulankhula modziteteza kuti:+
17 Koma iye anawakwezera dzanja+ kuti akhale chete, ndipo anawafotokozera mwatsatanetsatane mmene Yehova anamutulutsira m’ndende. Kenako iye anati: “Zinthu zimenezi mukazifotokoze kwa Yakobo+ ndi kwa abale.” Atatero anatuluka n’kupita kumalo ena.
40 Atamulola, Paulo anaimirira pamasitepe ndi kukwezera anthuwo dzanja.+ Onse atakhala phee, analankhula nawo m’Chiheberi,+ kuti:
26 Ndiyeno Agiripa+ anauza Paulo kuti: “Waloledwa kulankhula mbali yako.” Pamenepo Paulo anatambasula dzanja lake+ ndi kuyamba kulankhula modziteteza kuti:+