Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 13:55
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 55 Kodi si mwana wa mmisiri wamatabwa uyu?+ Kodi mayi ake si Mariya, ndipo abale ake si Yakobo, Yosefe, Simoni ndi Yudasi?

  • Machitidwe 15:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ataleka kulankhula, Yakobo anayankha kuti: “Amuna inu, abale anga, ndimvetsereni.+

  • Machitidwe 21:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Koma tsiku lotsatira, Paulo anapita nafe kwa Yakobo,+ ndipo akulu onse anali komweko.

  • 1 Akorinto 15:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kenako anaonekera kwa Yakobo,+ kenakonso kwa atumwi onse.+

  • Agalatiya 1:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Koma sindinaone mtumwi winanso kupatulapo Yakobo,+ m’bale+ wa Ambuye.

  • Agalatiya 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 iwo atazindikira kukoma mtima kwakukulu+ kumene ndinapatsidwa,+ Yakobo,+ Kefa ndi Yohane, amene anali ngati mizati,+ anagwira chanza ineyo ndi Baranaba.+ Anatero posonyeza kuti agwirizana nazo+ zoti ife tipite kwa anthu a mitundu ina, ndipo iwo apite kwa odulidwa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena