Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 12:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Koma iye anawakwezera dzanja+ kuti akhale chete, ndipo anawafotokozera mwatsatanetsatane mmene Yehova anamutulutsira m’ndende. Kenako iye anati: “Zinthu zimenezi mukazifotokoze kwa Yakobo+ ndi kwa abale.” Atatero anatuluka n’kupita kumalo ena.

  • Machitidwe 15:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ataleka kulankhula, Yakobo anayankha kuti: “Amuna inu, abale anga, ndimvetsereni.+

  • Agalatiya 1:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Koma sindinaone mtumwi winanso kupatulapo Yakobo,+ m’bale+ wa Ambuye.

  • Agalatiya 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 iwo atazindikira kukoma mtima kwakukulu+ kumene ndinapatsidwa,+ Yakobo,+ Kefa ndi Yohane, amene anali ngati mizati,+ anagwira chanza ineyo ndi Baranaba.+ Anatero posonyeza kuti agwirizana nazo+ zoti ife tipite kwa anthu a mitundu ina, ndipo iwo apite kwa odulidwa.

  • Yakobo 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Ine Yakobo,+ kapolo+ wa Mulungu ndi wa Ambuye Yesu Khristu, ndikupereka moni kwa mafuko 12+ amene ali obalalika:+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena