Mateyu 26:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 koma sanaupeze, ngakhale kuti kunabwera mboni zambiri zonama.+ Patapita nthawi, kunabwera mboni zina ziwiri Luka 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipotu ngakhale Herode sanam’peze ndi mlandu, n’chifukwa chake wam’bweza kwa ife. Ndithudi ameneyu sanachite chilichonse choyenera chilango cha imfa.+ Yohane 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pilato anatulukanso kunja ndi kuwauza kuti: “Onani! Ndikumutulutsa panja pano kwa inu, kuti mudziwe kuti sindikupeza mlandu mwa iye.”+
60 koma sanaupeze, ngakhale kuti kunabwera mboni zambiri zonama.+ Patapita nthawi, kunabwera mboni zina ziwiri
15 Ndipotu ngakhale Herode sanam’peze ndi mlandu, n’chifukwa chake wam’bweza kwa ife. Ndithudi ameneyu sanachite chilichonse choyenera chilango cha imfa.+
4 Pilato anatulukanso kunja ndi kuwauza kuti: “Onani! Ndikumutulutsa panja pano kwa inu, kuti mudziwe kuti sindikupeza mlandu mwa iye.”+