Aroma 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Anateronso kwa anthu amene anasinthanitsa choonadi+ cha Mulungu ndi bodza+ polambira chilengedwe ndi kuchichitira utumiki wopatulika m’malo mochita zimenezo kwa Iye amene anazilenga, amene ndi wotamandika kosatha. Ame. Akolose 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 pakuti zinthu zimenezo ndi mthunzi+ wa zimene zinali kubwera, koma zenizeni+ zake zili mwa Khristu.+
25 Anateronso kwa anthu amene anasinthanitsa choonadi+ cha Mulungu ndi bodza+ polambira chilengedwe ndi kuchichitira utumiki wopatulika m’malo mochita zimenezo kwa Iye amene anazilenga, amene ndi wotamandika kosatha. Ame.
17 pakuti zinthu zimenezo ndi mthunzi+ wa zimene zinali kubwera, koma zenizeni+ zake zili mwa Khristu.+