Genesis 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo iye anakhulupirira mwa Yehova,+ ndipo Mulunguyo anamuona Abulamu ngati wolungama.+ Agalatiya 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndithudi mukudziwa kuti amene amakhalabe ndi chikhulupiriro+ ndiwo ana a Abulahamu.+