Numeri 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mwamunayo akam’kaniza pa tsiku limene wamva kulonjezako,+ ndiye kuti wafafaniza lonjezo la mkaziyo, kapena lonjezo lake limene anachita mosaganizira bwino, limene analumbirira moyo wake ndi pakamwa pake. Yehova adzam’khululukira mkaziyo.+ 1 Akorinto 7:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Mkazi ndi womangika pa nthawi yonse imene mwamuna wake ali moyo.+ Komano mwamuna wake akamwalira, mkaziyo ndi womasuka kukwatiwa ndi aliyense amene akufuna, koma akwatiwe mwa Ambuye.+
8 Mwamunayo akam’kaniza pa tsiku limene wamva kulonjezako,+ ndiye kuti wafafaniza lonjezo la mkaziyo, kapena lonjezo lake limene anachita mosaganizira bwino, limene analumbirira moyo wake ndi pakamwa pake. Yehova adzam’khululukira mkaziyo.+
39 Mkazi ndi womangika pa nthawi yonse imene mwamuna wake ali moyo.+ Komano mwamuna wake akamwalira, mkaziyo ndi womasuka kukwatiwa ndi aliyense amene akufuna, koma akwatiwe mwa Ambuye.+