Aroma 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwachitsanzo, mkazi wokwatiwa amakhala womangidwa kwa mwamuna wake mwalamulo pamene mwamunayo ali moyo. Koma mwamuna wake akamwalira, mkazi amamasuka ku lamulo la mwamuna wake.+ 1 Akorinto 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma ndikufuna mudziwe kuti mutu wa mwamuna aliyense ndi Khristu.+ Mutu wa mkazi ndi mwamuna,+ ndipo mutu wa Khristu ndiye Mulungu.+ Aefeso 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Akazi agonjere+ amuna awo ngati mmene amagonjerera Ambuye,
2 Mwachitsanzo, mkazi wokwatiwa amakhala womangidwa kwa mwamuna wake mwalamulo pamene mwamunayo ali moyo. Koma mwamuna wake akamwalira, mkazi amamasuka ku lamulo la mwamuna wake.+
3 Koma ndikufuna mudziwe kuti mutu wa mwamuna aliyense ndi Khristu.+ Mutu wa mkazi ndi mwamuna,+ ndipo mutu wa Khristu ndiye Mulungu.+