Mika 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo alakalaka minda ya anthu ena ndipo ailanda.+ Alakalakanso nyumba za anthu ena n’kuzitenga kukhala zawo.+ Atenga mwachinyengo cholowa cha munthu ndi cha banja lake.+ Machitidwe 20:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Sindinasirire mwa nsanje siliva, golide kapena chovala cha munthu.+
2 Iwo alakalaka minda ya anthu ena ndipo ailanda.+ Alakalakanso nyumba za anthu ena n’kuzitenga kukhala zawo.+ Atenga mwachinyengo cholowa cha munthu ndi cha banja lake.+