Aroma 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chotero ngati kulakwa kwawo kukutanthauza chuma ku dziko, ndipo kuchepa kwawo kukutanthauza chuma kwa anthu a mitundu ina,+ bwanji nanga za chiwerengero chawo chokwanira?+ Chidzatanthauzatu zazikulu kuposa pamenepo! Chivumbulutso 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno ndinamva chiwerengero cha amene anadindidwa chidindo. Anthu okwana 144,000,+ ochokera m’fuko lililonse+ la ana a Isiraeli,+ anadindidwa chidindo:
12 Chotero ngati kulakwa kwawo kukutanthauza chuma ku dziko, ndipo kuchepa kwawo kukutanthauza chuma kwa anthu a mitundu ina,+ bwanji nanga za chiwerengero chawo chokwanira?+ Chidzatanthauzatu zazikulu kuposa pamenepo!
4 Ndiyeno ndinamva chiwerengero cha amene anadindidwa chidindo. Anthu okwana 144,000,+ ochokera m’fuko lililonse+ la ana a Isiraeli,+ anadindidwa chidindo: