Machitidwe 7:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 “Anthu okanika inu ndi osachita mdulidwe wa mumtima+ ndi m’makutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mmene anachitira makolo anu inunso mukuchita chimodzimodzi.+ Aheberi 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 musaumitse mitima yanu ngati mmene zinakhalira pamene makolo anu anandipsetsa mtima,+ ngati mmene zinalili pa tsiku la mayeso+ m’chipululu.+
51 “Anthu okanika inu ndi osachita mdulidwe wa mumtima+ ndi m’makutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mmene anachitira makolo anu inunso mukuchita chimodzimodzi.+
8 musaumitse mitima yanu ngati mmene zinakhalira pamene makolo anu anandipsetsa mtima,+ ngati mmene zinalili pa tsiku la mayeso+ m’chipululu.+