Mateyu 15:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 anatenga mitanda 7 ya mkate ija ndi nsomba zija. Atayamika, anainyemanyema n’kupatsa ophunzirawo ndipo iwo anagawira khamu la anthulo.+ 1 Timoteyo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndikutero chifukwa chakuti chilichonse cholengedwa ndi Mulungu n’chabwino,+ ndipo palibe chimene chiyenera kukanidwa+ ngati chalandiridwa moyamikira,+
36 anatenga mitanda 7 ya mkate ija ndi nsomba zija. Atayamika, anainyemanyema n’kupatsa ophunzirawo ndipo iwo anagawira khamu la anthulo.+
4 Ndikutero chifukwa chakuti chilichonse cholengedwa ndi Mulungu n’chabwino,+ ndipo palibe chimene chiyenera kukanidwa+ ngati chalandiridwa moyamikira,+