Luka 6:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 “Komanso, lekani kuweruza ena, mukatero inunso simudzaweruzidwa.+ Lekani kutsutsa ena, ndipo inunso simudzatsutsidwa. Pitirizani kukhululukira anthu machimo awo ndipo machimo anunso adzakhululukidwa.+ Aroma 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiwe ndani kuti uweruze wantchito wapakhomo wa mnzako?+ Ndi udindo wa bwana wake kumuweruza kuti ndi wolakwa kapena wosalakwa.+ Komatu Yehova akhoza kumukomera mtima chifukwa angathe kumuthandiza.+
37 “Komanso, lekani kuweruza ena, mukatero inunso simudzaweruzidwa.+ Lekani kutsutsa ena, ndipo inunso simudzatsutsidwa. Pitirizani kukhululukira anthu machimo awo ndipo machimo anunso adzakhululukidwa.+
4 Ndiwe ndani kuti uweruze wantchito wapakhomo wa mnzako?+ Ndi udindo wa bwana wake kumuweruza kuti ndi wolakwa kapena wosalakwa.+ Komatu Yehova akhoza kumukomera mtima chifukwa angathe kumuthandiza.+