Mateyu 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Lekani kuweruza ena+ kuti inunso musaweruzidwe, Aroma 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho munthu iwe,+ kaya ukhale ndani, ulibe chifukwa chomveka chodzilungamitsira ngati umaweruza ena.+ Pakuti pa nkhani imene ukuweruza nayo wina, ukudzitsutsa wekha, chifukwa iwenso woweruzawe+ umachita zomwezo.+ Aroma 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nanga n’chifukwa chiyani umaweruza m’bale wako?+ Kapenanso n’chifukwa chiyani umanyoza m’bale wako? Pakuti tonse tidzaimirira patsogolo pa mpando woweruzira milandu+ wa Mulungu.
2 Choncho munthu iwe,+ kaya ukhale ndani, ulibe chifukwa chomveka chodzilungamitsira ngati umaweruza ena.+ Pakuti pa nkhani imene ukuweruza nayo wina, ukudzitsutsa wekha, chifukwa iwenso woweruzawe+ umachita zomwezo.+
10 Nanga n’chifukwa chiyani umaweruza m’bale wako?+ Kapenanso n’chifukwa chiyani umanyoza m’bale wako? Pakuti tonse tidzaimirira patsogolo pa mpando woweruzira milandu+ wa Mulungu.