Aroma 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nanga n’chifukwa chiyani umaweruza m’bale wako?+ Kapenanso n’chifukwa chiyani umanyoza m’bale wako? Pakuti tonse tidzaimirira patsogolo pa mpando woweruzira milandu+ wa Mulungu. Yakobo 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Abale, muleke kunenerana zoipa.+ Wonenera m’bale wake zoipa kapena woweruza+ m’bale wake, akunenera zoipa lamulo ndi kuweruza lamulo. Choncho ngati ukuweruza lamulo, sukuchita zimene lamulo limanena ayi. Ukukhala woweruza.+
10 Nanga n’chifukwa chiyani umaweruza m’bale wako?+ Kapenanso n’chifukwa chiyani umanyoza m’bale wako? Pakuti tonse tidzaimirira patsogolo pa mpando woweruzira milandu+ wa Mulungu.
11 Abale, muleke kunenerana zoipa.+ Wonenera m’bale wake zoipa kapena woweruza+ m’bale wake, akunenera zoipa lamulo ndi kuweruza lamulo. Choncho ngati ukuweruza lamulo, sukuchita zimene lamulo limanena ayi. Ukukhala woweruza.+