Luka 6:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 “Komanso, lekani kuweruza ena, mukatero inunso simudzaweruzidwa.+ Lekani kutsutsa ena, ndipo inunso simudzatsutsidwa. Pitirizani kukhululukira anthu machimo awo ndipo machimo anunso adzakhululukidwa.+
37 “Komanso, lekani kuweruza ena, mukatero inunso simudzaweruzidwa.+ Lekani kutsutsa ena, ndipo inunso simudzatsutsidwa. Pitirizani kukhululukira anthu machimo awo ndipo machimo anunso adzakhululukidwa.+