Mateyu 27:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Komanso akazi ambiri ochokera ku Galileya amene ankatsatira Yesu kuti azimutumikira,+ anali komweko akuonerera chapatali ndithu.+ Luka 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Jowana+ mkazi wa Kuza kapitawo wa Herode, Suzana ndi amayi ena ambiri, amene anali kutumikira Yesu ndi atumwiwo pogwiritsa ntchito chuma chawo. Machitidwe 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndidzatsanuliranso mbali ya mzimu wanga ngakhale pa akapolo anga aamuna ndi aakazi m’masiku amenewo, ndipo iwo adzanenera.+
55 Komanso akazi ambiri ochokera ku Galileya amene ankatsatira Yesu kuti azimutumikira,+ anali komweko akuonerera chapatali ndithu.+
3 Jowana+ mkazi wa Kuza kapitawo wa Herode, Suzana ndi amayi ena ambiri, amene anali kutumikira Yesu ndi atumwiwo pogwiritsa ntchito chuma chawo.
18 Ndidzatsanuliranso mbali ya mzimu wanga ngakhale pa akapolo anga aamuna ndi aakazi m’masiku amenewo, ndipo iwo adzanenera.+