Mateyu 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Odala ndi anthu amene amazindikira zosowa zawo zauzimu,+ chifukwa ufumu wakumwamba ndi wawo.+ 1 Akorinto 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Komano munthu wauzimu+ amafufuza zinthu zonse, koma iye safufuzidwa+ ndi munthu aliyense. Akolose 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 N’chifukwa chake ifenso, kuyambira tsiku limene tinamva zimenezo, sitinaleke kukupemphererani.+ Takhala tikupemphanso kuti mukhale odziwa molondola+ chifuniro chake, ndiponso kuti mukhale ndi nzeru+ zonse komanso muzimvetsetsa zinthu zauzimu.+ Yuda 19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anthu amenewa ndiwo amayambitsa magawano,+ amachita zauchinyama,+ ndipo alibe mzimu wa Mulungu.+
9 N’chifukwa chake ifenso, kuyambira tsiku limene tinamva zimenezo, sitinaleke kukupemphererani.+ Takhala tikupemphanso kuti mukhale odziwa molondola+ chifuniro chake, ndiponso kuti mukhale ndi nzeru+ zonse komanso muzimvetsetsa zinthu zauzimu.+